-
Yeremiya 40:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nayenso Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a asilikali amene anali mʼdziko lonselo, anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa. 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.
-