Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 44:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndidzalanga anthu onse okhala mʼdziko la Iguputo ngati mmene ndinalangira Yerusalemu. Ndidzawalanga ndi lupanga, njala ndi mliri.*+

  • Ezekieli 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Gawo limodzi la magawo atatu a anthu a mtundu wako lidzafa ndi mliri* kapena lidzafa ndi njala pakati pako. Gawo lina lidzaphedwa ndi lupanga mokuzungulira.+ Gawo lachitatu ndidzalibalalitsira kumbali zonse, ndipo ndidzalithamangitsa nditasolola lupanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena