Yeremiya 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani. Ezekieli 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzayatsa moto mu Iguputo. Sini adzachita mantha kwambiri ndipo adani adzagumula mpanda wa No nʼkulowa mumzindamo. Adani adzaukira mzinda wa Nofi* dzuwa likuswa mtengo.
14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani.
16 Ndidzayatsa moto mu Iguputo. Sini adzachita mantha kwambiri ndipo adani adzagumula mpanda wa No nʼkulowa mumzindamo. Adani adzaukira mzinda wa Nofi* dzuwa likuswa mtengo.