Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mfumu Solomo inakondanso akazi ena ambiri a mitundu ina+ kuwonjezera pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi a Chimowabu,+ a Chiamoni,+ a Chiedomu, a Chisidoni+ ndi a Chihiti.+ 2 Akaziwa anali ochokera mʼmitundu imene Yehova anauza Aisiraeli kuti: “Musamakwatirane nawo komanso musamacheze nawo, chifukwa adzapotoza mitima yanu kuti muzitsatira milungu yawo.”+ Koma Solomo ankakonda anthu amenewa ndipo sanafune kuwasiya. 3 Iye anali ndi akazi olemekezeka 700 komanso akazi ena apambali 300 ndipo patapita nthawi, akaziwo anapotoza mtima wa Solomo.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena