-
Ezekieli 16:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 ‘Unamanga malo oti uzilambirirapo milungu yabodza ndipo unakonza malo okwera mʼbwalo lililonse la mzinda. 25 Unamanga malo ako okwerawo pamalo oonekera bwino kwambiri mumsewu uliwonse ndipo kukongola kwako unakusandutsa chinthu chonyansa podzipereka kwa munthu* aliyense wodutsa+ ndipo unachulukitsa zochita zako zauhulezo.+
-