-
1 Mafumu 9:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Nyumbayi idzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi adzayangʼana modabwa ndipo adzaimba mluzu nʼkunena kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira zimenezi dzikoli komanso nyumbayi?’+ 9 Ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chakuti anasiya Yehova Mulungu wawo amene anatulutsa makolo awo mʼdziko la Iguputo ndipo anatenga milungu ina nʼkumaigwadira ndi kuitumikira. Nʼchifukwa chake Yehova anawabweretsera tsoka lonseli.’”+
-