Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 48:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Imvani izi, inu a mʼnyumba ya Yakobo,

      Inu amene mumadzitchula dzina la Isiraeli+

      Ndiponso amene munatuluka kuchokera mʼmadzi a Yuda,*

      Inu amene mumalumbira pa dzina la Yehova+

      Ndiponso amene mumapemphera kwa Mulungu wa Isiraeli,

      Ngakhale kuti simuchita zimenezi kuchokera pansi pa mtima ndipo simuchita zoyenera.+

       2 Chifukwa mumanena kuti ndinu anthu amumzinda woyera+

      Ndipo mumadalira Mulungu wa Isiraeli+

      Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

  • Yeremiya 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ngakhale atalumbira kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo!”

      Adzakhalabe akulumbira mwachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena