Yeremiya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taona, lero ndakupatsa mphamvu pa mitundu ya anthu ndi maufumu, kuti uzule ndi kugwetsa, uwononge ndi kupasula, komanso kuti umange ndi kudzala.”+
10 Taona, lero ndakupatsa mphamvu pa mitundu ya anthu ndi maufumu, kuti uzule ndi kugwetsa, uwononge ndi kupasula, komanso kuti umange ndi kudzala.”+