Genesis 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno abale akewo anakhala pansi kuti adye chakudya. Koma atayangʼana, anaona gulu la Aisimaeli+ amene ankachokera ku Giliyadi. Ngamila zawo zinali zitanyamula zinthu zonunkhira monga labidanamu, basamu komanso makungwa a utomoni wonunkhira.+ Iwo anali pa ulendo wopita ku Iguputo. Yeremiya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+
25 Ndiyeno abale akewo anakhala pansi kuti adye chakudya. Koma atayangʼana, anaona gulu la Aisimaeli+ amene ankachokera ku Giliyadi. Ngamila zawo zinali zitanyamula zinthu zonunkhira monga labidanamu, basamu komanso makungwa a utomoni wonunkhira.+ Iwo anali pa ulendo wopita ku Iguputo.
22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+