1 Mafumu 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ahabu anapitadi kukadya ndiponso kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli ndipo anagwada nʼkuika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+
42 Ahabu anapitadi kukadya ndiponso kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli ndipo anagwada nʼkuika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+