-
Yeremiya 46:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 ‘Nʼchifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha?
Akubwerera ndipo asilikali awo agonjetsedwa.
Iwo athawa mwamantha ndipo asilikali awo sanacheuke.
Zochititsa mantha zili paliponse,’ akutero Yehova.
-
-
Yeremiya 46:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Nʼchifukwa chiyani amuna anu amphamvu akokoloka?
Iwo sanathe kulimba,
Chifukwa Yehova wawagonjetsa.
-