Nahumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni*+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anazunguliridwa ndi madzi.Nyanja inali chuma chake ndiponso khoma lake.
8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni*+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anazunguliridwa ndi madzi.Nyanja inali chuma chake ndiponso khoma lake.