Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu amene amakhulupirira munthu mnzake.+Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za munthu,+Komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova. Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ponena kuti, “Ayi, mʼmalomwake tipita kudziko la Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya. Ife tizikakhala kumeneko,”
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu amene amakhulupirira munthu mnzake.+Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za munthu,+Komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.
14 ponena kuti, “Ayi, mʼmalomwake tipita kudziko la Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya. Ife tizikakhala kumeneko,”