Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+ Yeremiya 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndiponso anthu a mitundu yosiyanasiyana. Mafumu onse amʼdziko la Uzi, mafumu onse amʼdziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza, Ekironi komanso amene anatsala ku Asidodi, Amosi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi,+Komanso wolamulira* wa ku Asikeloni.+Ndidzalanga Ekironi,+Ndipo ndidzafafaniza Afilisiti otsala,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’ Zefaniya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tsoka kwa anthu okhala mʼmbali mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, ndidzakuwononga,Moti mʼdziko lako simudzatsala munthu aliyense.
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+
20 ndiponso anthu a mitundu yosiyanasiyana. Mafumu onse amʼdziko la Uzi, mafumu onse amʼdziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza, Ekironi komanso amene anatsala ku Asidodi,
8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi,+Komanso wolamulira* wa ku Asikeloni.+Ndidzalanga Ekironi,+Ndipo ndidzafafaniza Afilisiti otsala,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’
5 “Tsoka kwa anthu okhala mʼmbali mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, ndidzakuwononga,Moti mʼdziko lako simudzatsala munthu aliyense.