Genesis 10:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+ Deuteronomo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Aavi ankakhala mʼmidzi mpaka kukafika ku Gaza.+ Iwo ankakhala mʼmidzi imeneyi mpaka pamene Akafitorimu+ ochokera ku Kafitori,* anawawononga nʼkuyamba kukhala mʼmidzi yawoyo.)
13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+
23 Koma Aavi ankakhala mʼmidzi mpaka kukafika ku Gaza.+ Iwo ankakhala mʼmidzi imeneyi mpaka pamene Akafitorimu+ ochokera ku Kafitori,* anawawononga nʼkuyamba kukhala mʼmidzi yawoyo.)