Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+ Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu amʼdzikoli adzafa, kaya ndi olemekezeka kapena onyozeka. Sadzaikidwa mʼmanda,Palibe aliyense amene adzalire maliro awo,Kapena kudzichekacheka komanso kumeta mpala chifukwa cha iwo.*
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu. Musamadzichekecheke+ kapena kumeta nsidze zanu* chifukwa cha anthu akufa.+
6 ‘Anthu amʼdzikoli adzafa, kaya ndi olemekezeka kapena onyozeka. Sadzaikidwa mʼmanda,Palibe aliyense amene adzalire maliro awo,Kapena kudzichekacheka komanso kumeta mpala chifukwa cha iwo.*