Genesis 19:36, 37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho ana a Loti awiri onsewo anakhala oyembekezera atagona ndi bambo awo. 37 Mwana woyamba anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndi tate wa Amowabu amasiku ano.+ Yesaya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Ari+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete. Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Kiri+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete.
36 Choncho ana a Loti awiri onsewo anakhala oyembekezera atagona ndi bambo awo. 37 Mwana woyamba anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndi tate wa Amowabu amasiku ano.+
15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Ari+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete. Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Kiri+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete.