Numeri 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, nʼkuthamangitsa Aamori amene anali kumeneko. Numeri 32:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo ana a Gadi anamanga* mizinda ya Diboni,+ Ataroti,+ Aroweli,+ 35 Atiroti-sofani, Yazeri,+ Yogebeha,+ Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
32 Kenako Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, nʼkuthamangitsa Aamori amene anali kumeneko.
34 Ndipo ana a Gadi anamanga* mizinda ya Diboni,+ Ataroti,+ Aroweli,+ 35 Atiroti-sofani, Yazeri,+ Yogebeha,+
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.