-
Numeri 21:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Anayamba kukhala kumeneko chifukwa Hesiboni unali mzinda wa Sihoni, mfumu ya Aamori, amene anamenyana ndi mfumu ya Mowabu nʼkulanda dziko lake lonse mpaka kukafika kuchigwa cha Arinoni.
-
-
Numeri 21:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chifukwa moto unatuluka ku Hesiboni, lawi lamoto linatuluka mʼtauni ya Sihoni.
Wawotcha Ari mzinda wa ku Mowabu, wawotcha olamulira amʼmalo okwezeka a ku Arinoni.
-