Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu nʼkusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumakona 4 a dziko lapansi.+ Yeremiya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼmasiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli.+ Onse pamodzi adzabwera kuchokera mʼdziko lakumpoto nʼkulowa mʼdziko limene ndinapereka kwa makolo anu kuti likhale cholowa chawo.+ Hoseya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ayuda ndi Aisiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzasankha mtsogoleri mmodzi nʼkutuluka mʼdzikolo chifukwa tsiku limeneli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.”+
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu nʼkusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumakona 4 a dziko lapansi.+
18 Mʼmasiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli.+ Onse pamodzi adzabwera kuchokera mʼdziko lakumpoto nʼkulowa mʼdziko limene ndinapereka kwa makolo anu kuti likhale cholowa chawo.+
11 Ayuda ndi Aisiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzasankha mtsogoleri mmodzi nʼkutuluka mʼdzikolo chifukwa tsiku limeneli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.”+