Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Aisiraeli adzabwerera nʼkuyamba kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndi Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera ndipo adzafunafuna ubwino wake mʼmasiku otsiriza.+
5 Kenako Aisiraeli adzabwerera nʼkuyamba kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndi Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera ndipo adzafunafuna ubwino wake mʼmasiku otsiriza.+