Yesaya 53:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonsefe tikungoyendayenda uku ndi uku ngati nkhosa zosochera.+Aliyense akulowera njira yakeNdipo Yehova wachititsa kuti zolakwa za tonsefe zigwere pa ameneyo.+
6 Tonsefe tikungoyendayenda uku ndi uku ngati nkhosa zosochera.+Aliyense akulowera njira yakeNdipo Yehova wachititsa kuti zolakwa za tonsefe zigwere pa ameneyo.+