Yesaya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana. Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.
18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana.
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.