Yesaya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso mofanana ndi ziweto zimene zilibe wozisonkhanitsa pamodzi,Aliyense adzabwerera kwa anthu ake.Aliyense adzathawira kudziko lake.+ Yeremiya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tinayesetsa kuti tichiritse Babulo koma sanachiritsike. Musiyeni, tiyeni tizipita. Aliyense apite kudziko lakwawo.+ Chifukwa zolakwa zake zafika kumwamba,Zafika pamwamba kwambiri ngati mitambo.+
14 Mofanana ndi insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso mofanana ndi ziweto zimene zilibe wozisonkhanitsa pamodzi,Aliyense adzabwerera kwa anthu ake.Aliyense adzathawira kudziko lake.+
9 “Tinayesetsa kuti tichiritse Babulo koma sanachiritsike. Musiyeni, tiyeni tizipita. Aliyense apite kudziko lakwawo.+ Chifukwa zolakwa zake zafika kumwamba,Zafika pamwamba kwambiri ngati mitambo.+