Yeremiya 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa tsiku lidzafika limene alonda amene ali mʼmapiri a Efuraimu adzafuula kuti: ‘Nyamukani, tiyeni tipite ku Ziyoni kwa Yehova Mulungu wathu.’”+
6 Chifukwa tsiku lidzafika limene alonda amene ali mʼmapiri a Efuraimu adzafuula kuti: ‘Nyamukani, tiyeni tipite ku Ziyoni kwa Yehova Mulungu wathu.’”+