Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+ Yeremiya 31:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena mʼbale wake kuti, ‘Mumʼdziwe Yehova!’+ chifukwa aliyense adzandidziwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+
34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena mʼbale wake kuti, ‘Mumʼdziwe Yehova!’+ chifukwa aliyense adzandidziwa kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+