Yesaya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu pamwamba pa nyenyezi za Mulungu,+Ndipo ndikhala paphiri lokumanapoKumapeto kwenikweni kwa madera akumpoto.+
13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu pamwamba pa nyenyezi za Mulungu,+Ndipo ndikhala paphiri lokumanapoKumapeto kwenikweni kwa madera akumpoto.+