Yesaya 13:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. 18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana.
17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. 18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana.