Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+