Yesaya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli. Chivumbulutso 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nʼchifukwa chake mʼtsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yake ndi imfa, kulira komanso njala ndipo adzapserera ndi moto+ chifukwa Yehova* Mulungu, amene anamuweruza ndi wamphamvu.+
14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.
8 Nʼchifukwa chake mʼtsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yake ndi imfa, kulira komanso njala ndipo adzapserera ndi moto+ chifukwa Yehova* Mulungu, amene anamuweruza ndi wamphamvu.+