Yeremiya 51:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Asilikali a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo akhala pansi mʼmalo awo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za mʼBabulo zawotchedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+
30 Asilikali a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo akhala pansi mʼmalo awo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za mʼBabulo zawotchedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+