-
Yesaya 13:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Kumeneko Mluya sadzakhomako tenti yake
Ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo.
21 Nyama zamʼchipululu zidzagona kumeneko.
Nyumba zawo zidzadzaza ndi akadzidzi.
-