Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+

  • Yeremiya 51:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Mizinda yake yakhala chinthu chochititsa mantha, dziko lopanda madzi komanso chipululu.

      Mizindayo yakhala dziko limene simudzakhalanso munthu aliyense ndipo palibe munthu amene adzadutsemo.+

  • Yeremiya 51:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire ndipo sadzatulukanso+ chifukwa cha tsoka limene ndikumugwetsera. Ndipo anthu amene akukhala mumzindawo adzatopa.’”+

      Mawu a Yeremiya athera pamenepa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena