Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+
19 Babulo, amene ndi waulemerero kwambiri* kuposa maufumu onse,+Chinthu chokongola chimene Akasidi amachinyadira,+Adzakhala ngati Sodomu ndi Gomora pa nthawi imene Mulungu anawononga mizindayi.+