Yesaya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+ Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide.
5 Iwo akubwera kuchokera kudziko lakutali,+Kuchokera kumalo akutali kwambiri pansi pa thambo,Yehova akubwera ndi zida zamkwiyo wake,Kuti awononge dziko lonse lapansi.+