Danieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo iye anachita mantha kwambiri. Miyendo komanso mawondo+ ake anayamba kunjenjemera.
6 Ndiyeno nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo iye anachita mantha kwambiri. Miyendo komanso mawondo+ ake anayamba kunjenjemera.