Yesaya 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndapatsa mphamvu winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+Iye adzachokera kotulukira dzuwa*+ ndipo adzaitana pa dzina langa. Adzapondaponda olamulira* ngati akuponda dongo+Ngati woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.
25 Ine ndapatsa mphamvu winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+Iye adzachokera kotulukira dzuwa*+ ndipo adzaitana pa dzina langa. Adzapondaponda olamulira* ngati akuponda dongo+Ngati woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.