Chivumbulutso 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mafumu a dziko lapansi amene anachita naye chiwerewere* nʼkumasangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa pomumvera chisoni, akadzaona utsi ukufuka chifukwa cha kupsa kwake.
9 Mafumu a dziko lapansi amene anachita naye chiwerewere* nʼkumasangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa pomumvera chisoni, akadzaona utsi ukufuka chifukwa cha kupsa kwake.