Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 22:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Anthu amʼdzikolo abera anthu mwachinyengo komanso achita zauchifwamba.+ Iwo achitira nkhanza anthu ovutika ndi osauka. Abera mlendo mwachinyengo komanso sanamuchitire zinthu mwachilungamo.’

  • Mika 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi.

      Pakati pa anthu palibe munthu wachilungamo.+

      Onse amabisalira anzawo kuti akhetse magazi.+

      Aliyense amasaka mʼbale wake ndi ukonde.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena