Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+ Yesaya 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+Tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Zolakwa zathu zili pa ife,Ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+ Ezekieli 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Oholiba anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule+ mpaka kufika pokumbukira masiku amene anali kamtsikana, pamene ankachita uhule mʼdziko la Iguputo.+
6 Kenako ndinanena kuti: “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi kuti ndikweze nkhope yanga kuyangʼana kwa inu Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu zachuluka kupitirira pamutu pathu ndipo machimo athu aunjikana mpaka kumwamba.+
12 Chifukwa zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+Tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Zolakwa zathu zili pa ife,Ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+
19 Oholiba anapitiriza kuwonjezera zochita zake zauhule+ mpaka kufika pokumbukira masiku amene anali kamtsikana, pamene ankachita uhule mʼdziko la Iguputo.+