-
Yeremiya 51:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Munthu aliyense akuchita zinthu mopanda nzeru komanso mosazindikira.
Mmisiri wa zitsulo aliyense adzachita manyazi chifukwa cha chifaniziro chake chosula.+
Chifukwa chifaniziro chake chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndi mulungu wonama
18 Iwo ndi achabechabe,+ oyenera kunyozedwa.
Tsiku loti aweruzidwe likadzafika adzawonongedwa.
-