Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova wanena kuti, ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto.+

      Iwo adzabwera ndipo aliyense adzakhazikitsa mpando wake wachifumu,

      Pakhomo la mageti a Yerusalemu.+

      Iwo adzaukira mpanda wake wonse

      Ndi mizinda yonse ya Yuda.+

  • Yeremiya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni.

      Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,”

      Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.

  • Yeremiya 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova wanena kuti:

      “Taonani! Anthu akubwera kuchokera kudziko lakumpoto.

      Ndipo mtundu wamphamvu udzadzutsidwa kuchokera kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi.+

  • Habakuku 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ine ndikubweretsa Akasidi,+

      Mtundu wankhanza ndiponso waphuma.

      Umene umathamanga mʼmadera ambiri apadziko lapansi,

      Kukalanda nyumba zimene si zawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena