Salimo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Yehova, musandidzudzule mutakwiya,Musandilangize mutapsa mtima.+ Salimo 38:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Inu Yehova, musandidzudzule mutakwiya,Kapena kundilangiza mutapsa mtima.+