Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaganizire mmene akuonekera komanso kutalika kwake+ chifukwa ine ndamukana ameneyu. Chifukwatu mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera. Munthu amaona zooneka ndi maso, koma Yehova amaona mumtima.”+

  • 1 Mbiri 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo iwe Solomo mwana wanga, dziwa Mulungu wa bambo wako ndipo uzimutumikira ndi mtima wonse+ komanso mosangalala, chifukwa Yehova amafufuza mitima yonse+ ndipo amazindikira maganizo a munthu ndi zolinga zake zonse.+ Ukamufunafuna, adzalola kuti umupeze,+ koma ukamusiya iye adzakusiya mpaka kalekale.+

  • Miyambo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+

      Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+

  • Miyambo 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Njira zonse za munthu zimaoneka zabwino kwa iye,+

      Koma Yehova amafufuza mitima.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena