-
Nehemiya 13:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno mthunzi utafika pamageti a Yerusalemu, Sabata lisanayambe, ndinalamula kuti zitseko zitsekedwe. Ndinalamulanso kuti asatsegule zitsekozo mpaka Sabata litatha. Ndipo ndinaika mʼmageti atumiki anga ena kuti katundu aliyense asalowe pa tsiku la Sabata.
-