Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 22:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Yehova wanena kuti, ‘Ndibweretsa tsoka pamalo ano ndiponso kwa anthu ake pokwaniritsa mawu onse amʼbuku limene mfumu ya Yuda yawerenga.+ 17 Chifukwa chakuti andisiya nʼkumapereka nsembe zautsi kwa milungu+ ina kuti andikwiyitse ndi ntchito zonse za manja awo,+ mkwiyo wanga udzayakira malo ano ndipo sudzazimitsidwa.’”+

  • Yesaya 65:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma inu muli mʼgulu la anthu amene asiya Yehova,+

      Anthu amene aiwala phiri langa loyera,+

      Amene amayalira tebulo mulungu wa Mwayi,

      Komanso amene amadzaza makapu ndi vinyo wosakaniza nʼkupereka kwa mulungu wa Zokonzedweratu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena