2 Mbiri 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ 2 Mbiri 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+
4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+