Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe* kwa Moleki.+ Usanyoze dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi.+ Ine ndine Yehova.

  • Yeremiya 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Iwo amanga malo okwera ku Tofeti, mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu,*+ kuti aziwotcha ana awo aamuna ndi ana awo aakazi pamoto,+ chinthu chimene sindinawalamule kuti azichita ndiponso chimene sindinachiganizirepo mumtima mwanga.’*+

  • Yeremiya 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kuwonjezera pamenepo, anamangira Baala malo okwera mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu*+ kuti aziwotcha* ana awo aamuna ndi ana awo aakazi pamoto ngati nsembe kwa Moleki.+ Ine sindinawalamule+ kuti azichita zimenezi. Ndipo sindinaganizirepo mumtima mwanga* zowauza kuti achite chinthu chonyansa chimenechi, chimene chachititsa kuti Yuda achimwe.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena