Yeremiya 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Choncho taonani! Masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti kapena kuti Chigwa cha Mwana wa Hinomu,* koma adzawatchula kuti Chigwa Chopherako Anthu. Iwo adzaika anthu mʼmanda ku Tofeti mpaka malo onse adzatha.+
32 ‘Choncho taonani! Masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti kapena kuti Chigwa cha Mwana wa Hinomu,* koma adzawatchula kuti Chigwa Chopherako Anthu. Iwo adzaika anthu mʼmanda ku Tofeti mpaka malo onse adzatha.+