Yeremiya 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi awo akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘Mfumukazi Yakumwamba.’*+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+ Yeremiya 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu adzabwera nʼkuyatsa mzindawu moti udzapseratu.+ Adzawotchanso nyumba zimene pamadenga ake anthu ankaperekerapo nsembe kwa Baala komanso nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+
18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi awo akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘Mfumukazi Yakumwamba.’*+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+
29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu adzabwera nʼkuyatsa mzindawu moti udzapseratu.+ Adzawotchanso nyumba zimene pamadenga ake anthu ankaperekerapo nsembe kwa Baala komanso nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+